17 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti:+ Amene wapambana pankhondo+ ndidzamupatsa ena mwa mana obisika+ komanso ndidzamupatsa mwala woyera. Pamwala woyerawo panalembedwa dzina latsopano limene wina aliyense sakulidziwa kupatulapo wolandira yekhayo.’