Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 16:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Aisiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “Nʼchiyani ichi?” chifukwa sankadziwa kuti chinali chiyani. Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+

  • Ekisodo 16:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Nyumba ya Isiraeli inapatsa chakudyacho dzina lakuti “mana.”* Chinali choyera ngati mapira,* ndipo kukoma kwake kunali ngati makeke opyapyala othira uchi.+

  • Salimo 78:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Iye anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.

      Anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+

  • Aheberi 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe+ ndi likasa la pangano+ lokutidwa ndi golide.+ Mulikasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana,+ ndodo ya Aroni imene inaphuka ija+ komanso miyala yosema+ ya pangano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena