Yesaya 47:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsoka lidzakugwera ndipo sudzatha kuliletsa ndi matsenga ako. Mavuto adzakugwera+ ndipo sudzatha kuwapewa. Chiwonongeko chimene sunali kuchiyembekezera chidzakupeza modzidzimutsa.+ Yeremiya 51:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 chifukwa Yehova akufunkha zinthu za Babulo ndi kuthetsa mawu ake aakulu.+ Mafunde awo adzachita phokoso ngati madzi ambiri.+ Komanso phokoso la mawu awo lidzamveka m’Babulo.
11 Koma tsoka lidzakugwera ndipo sudzatha kuliletsa ndi matsenga ako. Mavuto adzakugwera+ ndipo sudzatha kuwapewa. Chiwonongeko chimene sunali kuchiyembekezera chidzakupeza modzidzimutsa.+
55 chifukwa Yehova akufunkha zinthu za Babulo ndi kuthetsa mawu ake aakulu.+ Mafunde awo adzachita phokoso ngati madzi ambiri.+ Komanso phokoso la mawu awo lidzamveka m’Babulo.