Yesaya 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndani wapereka chigamulo+ chotsutsana ndi Turo, mzinda umene unali kuveka anthu zisoti zachifumu, umene amalonda ake anali akalonga, ndiponso umene ochita malonda ake anali anthu olemekezeka a padziko lapansi?+
8 Ndani wapereka chigamulo+ chotsutsana ndi Turo, mzinda umene unali kuveka anthu zisoti zachifumu, umene amalonda ake anali akalonga, ndiponso umene ochita malonda ake anali anthu olemekezeka a padziko lapansi?+