-
Genesis 41:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mʼmawa kutacha, Farao anavutika kwambiri maganizo. Choncho anaitanitsa ansembe onse amatsenga ndi amuna anzeru onse a mu Iguputo, nʼkuwafotokozera malotowo. Koma palibe amene anatha kumumasulira Farao maloto akewo.
-