-
Genesis 47:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Tiferenji ife inu mukuona, ndipo minda yathu ikhalirenji yogonera? Mutigule limodzi ndi minda yathu potipatsa chakudya kuti tikhale akapolo a Farao. Mutipatse tirigu kuti tikhale ndi moyo tisafe, komanso kuti minda yathu isagonere.”
-