Genesis 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno mwamunayo anati: “Tsopano uyu ndi fupa la mafupa angaKomanso mnofu wa mnofu wanga. Ameneyu azitchedwa Mkazi,Chifukwa anachokera kwa mwamuna.”+ Yesaya 45:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ineyo ndinapanga dziko lapansi+ ndipo ndinalenga munthu nʼkumuika padzikolo.+ Ndinatambasula kumwamba ndi manja angawa,+Ndipo zinthu zonse zimene zili kumwambako* ndimazipatsa malamulo.+ Mateyu 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yesu anayankha kuti: “Kodi simunawerenge kuti amene analenga anthu pachiyambi anawalenga mwamuna ndi mkazi+
23 Ndiyeno mwamunayo anati: “Tsopano uyu ndi fupa la mafupa angaKomanso mnofu wa mnofu wanga. Ameneyu azitchedwa Mkazi,Chifukwa anachokera kwa mwamuna.”+
12 Ineyo ndinapanga dziko lapansi+ ndipo ndinalenga munthu nʼkumuika padzikolo.+ Ndinatambasula kumwamba ndi manja angawa,+Ndipo zinthu zonse zimene zili kumwambako* ndimazipatsa malamulo.+
4 Yesu anayankha kuti: “Kodi simunawerenge kuti amene analenga anthu pachiyambi anawalenga mwamuna ndi mkazi+