Genesis 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Mulungu analenga munthu mʼchifaniziro chake, mʼchifaniziro cha Mulungu analenga munthu. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+ Genesis 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi.+ Pa tsiku limene anawalengalo,+ anawadalitsa nʼkuwatchula dzina lakuti Anthu.*
27 Choncho Mulungu analenga munthu mʼchifaniziro chake, mʼchifaniziro cha Mulungu analenga munthu. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+
2 Anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi.+ Pa tsiku limene anawalengalo,+ anawadalitsa nʼkuwatchula dzina lakuti Anthu.*