Genesis 42:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yosefe anapita kwayekha kukalira.+ Kenako anabwerako nʼkuyambiranso kulankhula nawo, ndipo anatenga Simiyoni+ nʼkumumanga iwo akuona.+
24 Ndiyeno Yosefe anapita kwayekha kukalira.+ Kenako anabwerako nʼkuyambiranso kulankhula nawo, ndipo anatenga Simiyoni+ nʼkumumanga iwo akuona.+