Genesis 42:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yosefe anapita payekha kukalira.+ Kenako anabwerako n’kuyambiranso kulankhula nawo, ndipo anatenga Simiyoni+ n’kumumanga iwo akuona.+
24 Ndiyeno Yosefe anapita payekha kukalira.+ Kenako anabwerako n’kuyambiranso kulankhula nawo, ndipo anatenga Simiyoni+ n’kumumanga iwo akuona.+