Yeremiya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi mu Giliyadi mulibe mafuta a basamu?+ Kapena kodi mulibe wochiritsa* mmenemo?+ Nʼchifukwa chiyani mwana wamkazi wa anthu anga sanachiritsidwe?+ Ezekieli 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yuda komanso dziko la Isiraeli linachita nawe malonda. Anakupatsa tirigu wa ku Miniti,+ zakudya zapamwamba, uchi,+ mafuta ndi basamu+ posinthanitsa ndi katundu wako.+
22 Kodi mu Giliyadi mulibe mafuta a basamu?+ Kapena kodi mulibe wochiritsa* mmenemo?+ Nʼchifukwa chiyani mwana wamkazi wa anthu anga sanachiritsidwe?+
17 Yuda komanso dziko la Isiraeli linachita nawe malonda. Anakupatsa tirigu wa ku Miniti,+ zakudya zapamwamba, uchi,+ mafuta ndi basamu+ posinthanitsa ndi katundu wako.+