Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano linafika tsiku limene ana a Mulungu woona*+ anapita kukaonekera pamaso pa Yehova,+ ndipo Satana+ nayenso anafika pakati pawo.+

  • Yobu 38:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pamene nyenyezi zamʼmawa+ zinafuula pamodzi mosangalala,

      Ndiponso pamene ana onse a Mulungu*+ anayamba kufuula mosangalala?

  • 2 Petulo 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndipotu Mulungu sanalekerere angelo amene anachimwa aja+ osawapatsa chilango. Koma anawaponya mu Tatalasi,*+ anawamanga mumdima wandiweyani podikira kuti adzawaweruze.+

  • Yuda 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiponso angelo amene anasiya utumiki umene Mulungu anawapatsa kumwamba komanso malo amene ankayenera kukhala,+ Mulungu anawamanga ndi maunyolo omwe sangaduke* nʼkuwasunga mumdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena