Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Mulungu anandionetsa Yoswa+ mkulu wa ansembe, ataimirira pamaso pa mngelo wa Yehova. Satana+ anali ataima kudzanja lamanja la Yoswa kuti azimutsutsa.

  • Mateyu 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako mzimu unatsogolera Yesu kuchipululu ndipo kumeneko anayesedwa+ ndi Mdyerekezi.+

  • Mateyu 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Woyesayo+ anabwera nʼkumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, uzani miyalayi kuti isanduke mitanda ya mkate.”

  • Luka 22:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Simoni, Simoni! Ndithu Satana akufuna kuti nonsenu akupeteni ngati tirigu.+

  • Yohane 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chakudya chamadzulo chinali chili mkati ndipo Mdyerekezi anali ataika kale maganizo ofuna kupereka Yesu+ mumtima mwa Yudasi Isikariyoti,+ mwana wa Simoni.

  • Chivumbulutso 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ imene imadziwika kuti Mdyerekezi+ komanso Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi kumene kuli anthu.+ Iye anaponyedwa padziko lapansi+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena