Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:14-16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako mmodzi wa ophunzira 12 aja, amene ankadziwika kuti Yudasi Isikariyoti,+ anapita kwa ansembe aakulu+ 15 nʼkuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+ 16 Choncho kuyambira nthawi imeneyo anayesetsa kufunafuna mpata wabwino kuti amupereke.

  • Mateyu 26:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Zoonadi, Mwana wa munthu achoka, mogwirizana ndi zimene Malemba amanena za iye. Koma tsoka+ kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino kwa munthu ameneyu ngati akanapanda kubadwa.”+

  • Maliko 14:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Yudasi Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anachoka nʼkupita kwa ansembe aakulu kuti akapereke Yesu kwa iwo.+ 11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndipo anamulonjeza kuti amupatsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino kuti amupereke.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena