Genesis 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho zamoyo zonse zoyenda padziko lapansi, monga zamoyo zouluka, nyama zoweta, nyama zakutchire, ndiponso tizilombo tonse tingʼonotingʼono toyenda mʼmagulu, zinafa+ pamodzi ndi anthu onse.+ Salimo 104:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukabisa nkhope yanu, zimasokonezeka. Mukachotsa mzimu wawo,* zimafa ndipo zimabwerera kufumbi.+ Mateyu 24:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anthu ananyalanyaza zimene zinkachitika mpaka Chigumula chinafika nʼkuwaseseratu onsewo.+ Zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu. 2 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu sanalekerere dziko lakale lija osalipatsa chilango,+ koma anasunga Nowa, yemwe ankalalikira za chilungamo cha Mulungu.+ Anamupulumutsa limodzi ndi anthu enanso 7,+ pamene anabweretsa chigumula padziko la anthu osaopa Mulungu.+
21 Choncho zamoyo zonse zoyenda padziko lapansi, monga zamoyo zouluka, nyama zoweta, nyama zakutchire, ndiponso tizilombo tonse tingʼonotingʼono toyenda mʼmagulu, zinafa+ pamodzi ndi anthu onse.+
39 Anthu ananyalanyaza zimene zinkachitika mpaka Chigumula chinafika nʼkuwaseseratu onsewo.+ Zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.
5 Mulungu sanalekerere dziko lakale lija osalipatsa chilango,+ koma anasunga Nowa, yemwe ankalalikira za chilungamo cha Mulungu.+ Anamupulumutsa limodzi ndi anthu enanso 7,+ pamene anabweretsa chigumula padziko la anthu osaopa Mulungu.+