Genesis 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndi Ahori+ kuphiri lawo la Seiri,+ mpaka kukafika ku Eli-parana, kuchipululu. Deuteronomo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyamba, Ahori+ ankakhala ku Seiri, koma mbadwa za Esau zinawalanda dzikolo nʼkuwapha ndipo iwo anayamba kukhala mʼdzikolo,+ mofanana ndi zimene Aisiraeli adzachite ndi dziko limene ndi cholowa chawo, limene Yehova adzawapatsadi.) Deuteronomo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu anachitanso zimenezi kwa mbadwa za Esau zimene zikukhala ku Seiri.+ Iye anagonjetsa Ahori+ pamaso pawo kuti mbadwa za Esauzo zitenge dzikolo nʼkumakhalamo mpaka lero.
12 Poyamba, Ahori+ ankakhala ku Seiri, koma mbadwa za Esau zinawalanda dzikolo nʼkuwapha ndipo iwo anayamba kukhala mʼdzikolo,+ mofanana ndi zimene Aisiraeli adzachite ndi dziko limene ndi cholowa chawo, limene Yehova adzawapatsadi.)
22 Mulungu anachitanso zimenezi kwa mbadwa za Esau zimene zikukhala ku Seiri.+ Iye anagonjetsa Ahori+ pamaso pawo kuti mbadwa za Esauzo zitenge dzikolo nʼkumakhalamo mpaka lero.