Ekisodo 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aroni+ aziwotcha zofukiza zonunkhira+ kuti paguwapo+ pazikhala utsi mʼmawa uliwonse akamasamalira nyale.+ Ekisodo 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno udzaike guwa lansembe zofukiza lagolide+ patsogolo pa likasa la Umboni, nʼkuika nsalu yotchinga pakhomo la chihema.+ Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale ngati zofukiza+ zokonzedwa pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+ Chivumbulutso 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mngelo wina anafika atanyamula chiwiya chofukizira chagolide nʼkuima paguwa lansembe.+ Iye anapatsidwa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide,+ limene linali pamaso pa mpando wachifumu.
7 Aroni+ aziwotcha zofukiza zonunkhira+ kuti paguwapo+ pazikhala utsi mʼmawa uliwonse akamasamalira nyale.+
5 Ndiyeno udzaike guwa lansembe zofukiza lagolide+ patsogolo pa likasa la Umboni, nʼkuika nsalu yotchinga pakhomo la chihema.+
2 Pemphero langa likhale ngati zofukiza+ zokonzedwa pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
3 Mngelo wina anafika atanyamula chiwiya chofukizira chagolide nʼkuima paguwa lansembe.+ Iye anapatsidwa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide,+ limene linali pamaso pa mpando wachifumu.