Ekisodo 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako mupange choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Choikapo nyalecho chikhale chinthu chimodzi chosula ndipo chikhale ndi tsinde, thunthu, nthambi, timasamba tamʼmunsi mwa duwa, mphindi ndi maluwa.+ Aheberi 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa panamangidwa chipinda choyamba cha chihema ndipo mʼchipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo ndi mikate yoonetsa kwa Mulungu,*+ ndipo chinkatchedwa “Malo Oyera.”+
31 Kenako mupange choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Choikapo nyalecho chikhale chinthu chimodzi chosula ndipo chikhale ndi tsinde, thunthu, nthambi, timasamba tamʼmunsi mwa duwa, mphindi ndi maluwa.+
2 Chifukwa panamangidwa chipinda choyamba cha chihema ndipo mʼchipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo ndi mikate yoonetsa kwa Mulungu,*+ ndipo chinkatchedwa “Malo Oyera.”+