Levitiko 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni ndipo anawaveka mikanjo, anawamanga malamba apamimba komanso anawakulunga mipango kumutu,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni ndipo anawaveka mikanjo, anawamanga malamba apamimba komanso anawakulunga mipango kumutu,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.