Levitiko 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo Mose anatenga ena mwa mafuta odzozera+ ndi magazi amene anali paguwa lansembe aja nʼkuwaza Aroni ndi zovala zake komanso ana ake ndi zovala zawo. Choncho anapatula Aroni ndi zovala zake komanso ana ake+ ndi zovala zawo.+
30 Ndipo Mose anatenga ena mwa mafuta odzozera+ ndi magazi amene anali paguwa lansembe aja nʼkuwaza Aroni ndi zovala zake komanso ana ake ndi zovala zawo. Choncho anapatula Aroni ndi zovala zake komanso ana ake+ ndi zovala zawo.+