Ekisodo 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Upangenso nsalu za ubweya wa mbuzi+ zoyala pachihemacho. Nsaluzo zikhale zokwana 11.+