Ekisodo 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo patebulopo muziikapo mkate wachionetsero pamaso panga nthawi zonse.+ Mateyu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye analowa mʼnyumba ya Mulungu ndipo anadya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,*+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sankayenera kudya malinga ndi malamulo, koma ansembe okha.+
4 Iye analowa mʼnyumba ya Mulungu ndipo anadya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,*+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sankayenera kudya malinga ndi malamulo, koma ansembe okha.+