Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Musamabe,+ musamapusitse anzanu+ ndiponso musamachitirane chinyengo.

  • Deuteronomo 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Musabe.+

  • Maliko 10:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iwe umadziwa malamulo akuti: ‘Musaphe munthu,*+ musachite chigololo,+ musabe,+ musapereke umboni wabodza,+ musabere munthu mwachinyengo+ ndiponso lakuti muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’”+

  • 1 Akorinto 6:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu Ufumu wa Mulungu?+ Musapusitsidwe.* Achiwerewere,*+ olambira mafano,+ achigololo,+ amuna amene amalola kugonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+ 10 akuba, adyera,+ zidakwa,+ olalata, kapena olanda, onsewo sadzalowa mu Ufumu wa Mulungu.+

  • Aefeso 4:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Munthu wakuba asiye kubako, koma azigwira ntchito molimbikira. Azigwira ntchito yabwino ndi manja ake+ kuti azitha kupeza zinthu zimene angathe kugawana ndi munthu wosowa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena