Machitidwe 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ameneyu ndi amene anali ndi Aisiraeli mʼchipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu+ komanso makolo athu paphiri la Sinai. Iye analandira mawu opatulika omwe ndi amphamvu kuti atipatsire.+ Agalatiya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye nʼchifukwa chiyani Chilamulo chinaperekedwa? Anatipatsa Chilamulochi kuti machimo aonekere,+ mpaka mbadwa* imene inapatsidwa lonjezolo itafika.+ Angelo anapereka Chilamulocho+ kudzera mʼdzanja la mkhalapakati.+
38 Ameneyu ndi amene anali ndi Aisiraeli mʼchipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu+ komanso makolo athu paphiri la Sinai. Iye analandira mawu opatulika omwe ndi amphamvu kuti atipatsire.+
19 Ndiye nʼchifukwa chiyani Chilamulo chinaperekedwa? Anatipatsa Chilamulochi kuti machimo aonekere,+ mpaka mbadwa* imene inapatsidwa lonjezolo itafika.+ Angelo anapereka Chilamulocho+ kudzera mʼdzanja la mkhalapakati.+