Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 37:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Atatero anapanga ziwiya zapatebulolo, mbale zake, makapu, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Anazipanga ndi golide woyenga bwino.+

  • Numeri 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iwo aziyalanso nsalu yabuluu patebulo la mkate wachionetsero,+ nʼkuikapo mbale, makapu, mbale zolowa ndi mitsuko ya nsembe yachakumwa.+ Mkate wachionetsero+ womwe ndi nsembe ya nthawi zonse uzikhalabe pomwepo.

  • 1 Mafumu 7:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Solomo anapanga zinthu zonse zapanyumba ya Yehova. Anapanga guwa lansembe+ lagolide komanso tebulo yagolide+ yoikapo mkate wachionetsero.

  • 1 Mafumu 7:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 mabeseni, zozimitsira nyale,+ mbale zolowa, makapu+ ndiponso zopalira moto.+ Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino. Anapanganso molowa miyendo ya zitseko za chipinda chamkati,+ kutanthauza Malo Oyera Koposa ndiponso molowa miyendo ya zitseko za nyumbayo.+ Zonsezi zinali zagolide.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena