Ekisodo 25:23, 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mupangenso tebulo+ la mtengo wa mthethe, masentimita 90 mulitali, masentimita 45 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi mpaka mʼmwamba.+ 24 Mudzalikute ndi golide woyenga bwino, ndipo mudzapange mkombero wagolide kuzungulira tebulo lonselo.
23 Mupangenso tebulo+ la mtengo wa mthethe, masentimita 90 mulitali, masentimita 45 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi mpaka mʼmwamba.+ 24 Mudzalikute ndi golide woyenga bwino, ndipo mudzapange mkombero wagolide kuzungulira tebulo lonselo.