Numeri 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choikapo nyalecho anachipanga chonchi: Chinali chagolide komanso chosula+ kuchokera kutsinde lake mpaka kumaluwa ake. Choikapo nyalecho anachipanga mogwirizana ndi chitsanzo chimene Yehova anaonetsa Mose mʼmasomphenya.+
4 Choikapo nyalecho anachipanga chonchi: Chinali chagolide komanso chosula+ kuchokera kutsinde lake mpaka kumaluwa ake. Choikapo nyalecho anachipanga mogwirizana ndi chitsanzo chimene Yehova anaonetsa Mose mʼmasomphenya.+