Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Mose anakwera mʼphirimo kukaonekera kwa Mulungu woona.+ Ndipo Yehova analankhula naye mʼphirimo kuti: “Ukanene mawu awa kunyumba ya Yakobo kapena kuti kwa Aisiraeli,

  • Ekisodo 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mukapange chihema chopatulika ndi ziwiya zake zonse mogwirizana ndendende ndi zimene ndikukusonyeza.+

  • Machitidwe 7:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Makolo athuwo anali ndi chihema cha umboni mʼchipululu. Anachipanga potsatira malangizo amene Mulungu anapereka kwa Mose mogwirizana ndi chithunzi chimene Moseyo anachiona.+

  • Aheberi 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Utumiki umene amuna amenewa akuchita uli ngati chifaniziro ndiponso chithunzi+ cha zinthu zakumwamba.+ Izi zikufanana ndi lamulo limene Mulungu anapatsa Mose atatsala pangʼono kumanga chihema. Lamulo lake linali lakuti: “Uonetsetse kuti wapanga zinthu zonse motsatira chitsanzo chimene wasonyezedwa mʼphiri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena