Ekisodo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mukapange chihema chopatulika ndi ziwiya zake zonse mogwirizana ndendende ndi zimene ndikukusonyeza.+ Ekisodo 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Uonetsetse kuti wazipanga motsatira chitsanzo chimene wasonyezedwa mʼphiri.”+ Ekisodo 26:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Upange chihemacho motsatira pulani yake imene ndakuonetsa mʼphiri.+ Numeri 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choikapo nyalecho anachipanga chonchi: Chinali chagolide komanso chosula+ kuchokera kutsinde lake mpaka kumaluwa ake. Choikapo nyalecho anachipanga mogwirizana ndi chitsanzo chimene Yehova anaonetsa Mose mʼmasomphenya.+
9 Mukapange chihema chopatulika ndi ziwiya zake zonse mogwirizana ndendende ndi zimene ndikukusonyeza.+
4 Choikapo nyalecho anachipanga chonchi: Chinali chagolide komanso chosula+ kuchokera kutsinde lake mpaka kumaluwa ake. Choikapo nyalecho anachipanga mogwirizana ndi chitsanzo chimene Yehova anaonetsa Mose mʼmasomphenya.+