-
1 Mafumu 8:64Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
64 Tsiku limenelo, mfumu inapatula pakati pa bwalo la nyumba ya Yehova chifukwa inkafunika kuperekerapo nsembe zopsereza, nsembe zambewu komanso mafuta a nsembe zamgwirizano. Inachita zimenezi chifukwa guwa lansembe lakopa*+ lapatsogolo pa kachisi wa Yehova linali lalingʼono kwambiri moti nsembe zopsereza, nsembe zambewu ndiponso mafuta+ a nsembe zamgwirizano sizikanakwanapo.
-