Ekisodo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Upangenso kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti: ‘Yehova ndi Woyera.’+ Ekisodo 39:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Yehova ndi Woyera.” Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+ Levitiko 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anamuvekanso nduwira+ kumutu kwake, nʼkuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
36 Upangenso kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti: ‘Yehova ndi Woyera.’+
30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Yehova ndi Woyera.” Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+
9 Anamuvekanso nduwira+ kumutu kwake, nʼkuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.