Ekisodo 28:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ana a Aroni uwapangirenso mikanjo, malamba ndi mipango* yokulunga kumutu+ kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+ Levitiko 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni ndipo anawaveka mikanjo, anawamanga malamba apamimba komanso anawakulunga mipango kumutu,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
40 Ana a Aroni uwapangirenso mikanjo, malamba ndi mipango* yokulunga kumutu+ kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+
13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni ndipo anawaveka mikanjo, anawamanga malamba apamimba komanso anawakulunga mipango kumutu,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.