Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano lamulo la nsembe yamgwirizano+ imene aliyense azipereka kwa Yehova ndi ili: Levitiko 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa zinthu zimenezi azipereka mtanda umodzi wa nsembe iliyonse kuti ikhale gawo lopatulika loperekedwa kwa Yehova. Mtandawo uzikhala wa wansembe amene wawaza magazi a nsembe zamgwirizanozo paguwa lansembe.+
14 Pa zinthu zimenezi azipereka mtanda umodzi wa nsembe iliyonse kuti ikhale gawo lopatulika loperekedwa kwa Yehova. Mtandawo uzikhala wa wansembe amene wawaza magazi a nsembe zamgwirizanozo paguwa lansembe.+