31 Ndiyeno Mose anauza Aroni ndi ana ake kuti: “Wiritsani+ nyamayo pakhomo la chihema chokumanako, ndipo muidyerenso pomwepo pamodzi ndi mkate umene uli mʼdengu logwiritsidwa ntchito poika anthu kuti akhale ansembe, mogwirizana ndi zimene anandilamula kuti, ‘Aroni ndi ana ake adye zimenezi.’+