Levitiko 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wamba* asadye chinthu chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala mʼnyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chinthu chopatulika chilichonse. Numeri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe, ndipo azigwira ntchito zawo zaunsembe.+ Munthu wamba* aliyense amene wayandikira malowo, aziphedwa.”+
10 Munthu wamba* asadye chinthu chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala mʼnyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chinthu chopatulika chilichonse.
10 Uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe, ndipo azigwira ntchito zawo zaunsembe.+ Munthu wamba* aliyense amene wayandikira malowo, aziphedwa.”+