-
Levitiko 8:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mose anachita mogwirizana ndi zimene Yehova anamulamula. Ndipo gulu lonse linasonkhana pakhomo la chihema chokumanako.
-