Ekisodo 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wansembe amene adzalowe mʼmalo mwake kuchokera pakati pa ana ake, amene adzalowe mʼchihema chokumanako kukatumikira mʼmalo oyera, azidzavala zovalazo kwa masiku 7.+ Ekisodo 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Uchite zimenezi kwa Aroni ndi ana ake malinga ndi zonse zimene ndakulamula. Udzatenga masiku 7 kuti uwaike* kukhala ansembe.+ Numeri 3:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mayina a ana a Aroni anali awa: woyamba Nadabu kenako Abihu,+ Eleazara+ ndi Itamara.+ 3 Ana a Aroni mayina awo anali amenewa. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anaikidwa* kuti akhale ansembe.+
30 Wansembe amene adzalowe mʼmalo mwake kuchokera pakati pa ana ake, amene adzalowe mʼchihema chokumanako kukatumikira mʼmalo oyera, azidzavala zovalazo kwa masiku 7.+
35 Uchite zimenezi kwa Aroni ndi ana ake malinga ndi zonse zimene ndakulamula. Udzatenga masiku 7 kuti uwaike* kukhala ansembe.+
2 Mayina a ana a Aroni anali awa: woyamba Nadabu kenako Abihu,+ Eleazara+ ndi Itamara.+ 3 Ana a Aroni mayina awo anali amenewa. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anaikidwa* kuti akhale ansembe.+