Numeri 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amenewa ndiwo anali mayina a ana a Aroni. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anapatsidwa mphamvu* yotumikira monga ansembe.+
3 Amenewa ndiwo anali mayina a ana a Aroni. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anapatsidwa mphamvu* yotumikira monga ansembe.+