Ekisodo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Pakati pa Aisiraeli, usankhe Aroni+ mʼbale wako pamodzi ndi ana ake+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara komanso Itamara+ kuti atumikire monga ansembe anga. Levitiko 8:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tenga Aroni limodzi ndi ana ake,+ zovala zawo,+ mafuta odzozera,+ ngʼombe yamphongo ya nsembe yamachimo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi dengu la mikate yopanda zofufumitsa.+ 3 Ndiyeno usonkhanitse gulu lonse pakhomo la chihema chokumanako.”
28 “Pakati pa Aisiraeli, usankhe Aroni+ mʼbale wako pamodzi ndi ana ake+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara komanso Itamara+ kuti atumikire monga ansembe anga.
2 “Tenga Aroni limodzi ndi ana ake,+ zovala zawo,+ mafuta odzozera,+ ngʼombe yamphongo ya nsembe yamachimo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi dengu la mikate yopanda zofufumitsa.+ 3 Ndiyeno usonkhanitse gulu lonse pakhomo la chihema chokumanako.”