Ekisodo 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo Eleazara+ mwana wa Aroni, anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anamʼberekera Pinihasi.+ Amenewa ndi atsogoleri a mabanja amʼfuko la Levi, mogwirizana ndi mabanja awo.+ Deuteronomo 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero Aisiraeli anachoka ku Beeroti Bene-yaakana kupita ku Mosera. Kumeneku nʼkumene Aroni anafera ndipo anamuikanso komweko.+ Mwana wake Eleazara anayamba kutumikira monga wansembe mʼmalo mwa Aroniyo.+
25 Ndipo Eleazara+ mwana wa Aroni, anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anamʼberekera Pinihasi.+ Amenewa ndi atsogoleri a mabanja amʼfuko la Levi, mogwirizana ndi mabanja awo.+
6 Zitatero Aisiraeli anachoka ku Beeroti Bene-yaakana kupita ku Mosera. Kumeneku nʼkumene Aroni anafera ndipo anamuikanso komweko.+ Mwana wake Eleazara anayamba kutumikira monga wansembe mʼmalo mwa Aroniyo.+