Ekisodo 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wansembe amene adzalowa m’malo mwake kuchokera pakati pa ana ake, amene adzalowa m’chihema chokumanako kukatumikira m’malo oyera azidzavala zovalazo kwa masiku 7.+
30 Wansembe amene adzalowa m’malo mwake kuchokera pakati pa ana ake, amene adzalowa m’chihema chokumanako kukatumikira m’malo oyera azidzavala zovalazo kwa masiku 7.+