Ekisodo 40:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako mtambo unayamba kuphimba chihema chokumanako ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza mʼchihemacho.+ Numeri 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita. 1 Mafumu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo analephera kutumikira popeza ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+
34 Kenako mtambo unayamba kuphimba chihema chokumanako ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza mʼchihemacho.+
5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita.
11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo analephera kutumikira popeza ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+