15 Pa tsiku limene anamanga chihema,+ mtambo unaima pamwamba pa chihema cha Umbonicho. Koma kuyambira madzulo mpaka mʼmamawa, moto unkaoneka pamwamba pa chihemacho.+
8 Mʼmalo opatulikawo munadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa mʼmalo opatulikawo mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.