Ekisodo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, udzamange chihema kapena kuti chihema chokumanako.+ Ekisodo 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho mʼmwezi woyamba wa chaka chachiwiri, pa tsiku loyamba la mweziwo, anamanga chihema.+