Ekisodo 40:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako mtambo unayamba kuphimba chihema chokumanako ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza mʼchihemacho.+ Ekisodo 40:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mtambo wa Yehova unkakhala pamwamba pa chihema masana ndipo usiku pankakhala moto. Nyumba yonse ya Isiraeli inkaona zimenezi mʼzigawo zonse za ulendo wawo.+
34 Kenako mtambo unayamba kuphimba chihema chokumanako ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza mʼchihemacho.+
38 Mtambo wa Yehova unkakhala pamwamba pa chihema masana ndipo usiku pankakhala moto. Nyumba yonse ya Isiraeli inkaona zimenezi mʼzigawo zonse za ulendo wawo.+