Ekisodo 40:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mtambo wa Yehovawo unali kukhala pamwamba pa chihema chopatulika usana, ndipo usiku panali kukhala moto. Nyumba yonse ya Isiraeli inali kuona zimenezi m’zigawo zonse za ulendo wawo.+
38 Mtambo wa Yehovawo unali kukhala pamwamba pa chihema chopatulika usana, ndipo usiku panali kukhala moto. Nyumba yonse ya Isiraeli inali kuona zimenezi m’zigawo zonse za ulendo wawo.+