Ekisodo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+ Numeri 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zinali kuchitika motero nthawi zonse. Mtambo unali kuima pamwamba pa chihemacho masana, ndipo usiku moto unali kuonekera pamwamba pake.+ Salimo 78:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+
21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+
16 Zinali kuchitika motero nthawi zonse. Mtambo unali kuima pamwamba pa chihemacho masana, ndipo usiku moto unali kuonekera pamwamba pake.+
14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+