Numeri 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zimenezi ndi zomwe zinkachitika nthawi zonse. Mtambo unkaima pamwamba pa chihemacho masana ndipo usiku pankaoneka moto.+
16 Zimenezi ndi zomwe zinkachitika nthawi zonse. Mtambo unkaima pamwamba pa chihemacho masana ndipo usiku pankaoneka moto.+