Ekisodo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chipilala cha mtambo sichinkachoka patsogolo pa anthuwo masana, komanso chipilala cha moto sichinkachoka patsogolo pawo usiku.+ Nehemiya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 inu simunawasiye mʼchipululu, chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+ Chipilala cha mtambo sichinawachokere masana ndipo chinkawatsogolera, komanso chipilala cha moto sichinawachokere usiku ndipo chinkawaunikira njira yoyenera kudutsa.+
22 Chipilala cha mtambo sichinkachoka patsogolo pa anthuwo masana, komanso chipilala cha moto sichinkachoka patsogolo pawo usiku.+
19 inu simunawasiye mʼchipululu, chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+ Chipilala cha mtambo sichinawachokere masana ndipo chinkawatsogolera, komanso chipilala cha moto sichinawachokere usiku ndipo chinkawaunikira njira yoyenera kudutsa.+