Numeri 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zinali kuchitika motero nthawi zonse. Mtambo unali kuima pamwamba pa chihemacho masana, ndipo usiku moto unali kuonekera pamwamba pake.+
16 Zinali kuchitika motero nthawi zonse. Mtambo unali kuima pamwamba pa chihemacho masana, ndipo usiku moto unali kuonekera pamwamba pake.+